Chichewa Language

Nthano ya Chipulumutso

Download


Pa mtanda Yesu munafera
Munauka, kuombola otayika
Khululukani machimo anga
Idzani Yesu ndinu zanga zonse
Sinthani moyo wanga, mundilengenso
Ndifunitsa kuyenda nanu

All Versions & Translations